Zoyenereza kuti anthu a kwatirane kapena kulowa m’banja Zitsanzo za Migwirizano

Zoyenereza kuti anthu a kwatirane kapena kulowa m’banja. Munthu wa mkazi ndi wa mwamuna amene ali ndi zaka zosachepera 18 zakubadwa komanso amene ubongo wawo umagwira ntchito ndi ovomerezedwa ndi lamulo kukwatilana. Izi zikutanthauza kuti: